-
2 Mbiri 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mfumu Solomo inapereka nsembe ngʼombe 22,000 ndi nkhosa 120,000. Choncho mfumuyo ndi anthu onse anatsegulira nyumba ya Mulungu woona.+
-