Genesis 35:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Numeri 2:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Aseri. Mtsogoleri wa ana a Aseri ndi Pagiyeli,+ mwana wa Okirani. 28 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 41,500.+
27 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Aseri. Mtsogoleri wa ana a Aseri ndi Pagiyeli,+ mwana wa Okirani. 28 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 41,500.+