Numeri 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Amene azimanga msasa wawo kumpoto ndi gulu la mafuko atatu la Dani ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Dani ndi Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai. Numeri 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
25 Amene azimanga msasa wawo kumpoto ndi gulu la mafuko atatu la Dani ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Dani ndi Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.