-
Levitiko 4:22, 23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ngati mtsogoleri+ wachimwa mosadziwa pochita chimodzi mwa zinthu zonse zimene Yehova Mulungu wake analamula kuti asachite ndipo wapalamula, 23 kapena ngati wadziwa kuti wachimwa pochita zinthu zosemphana ndi lamulo, azibweretsa mbuzi yaingʼono yamphongo yopanda chilema, kuti ikhale nsembe yake.
-