Ekisodo 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Samueli 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene amakhala pamwamba* pa akerubi.+ Ana awiri a Eli, Hofeni ndi Pinihasi,+ analinso komweko limodzi ndi likasa la pangano la Mulungu woona. Salimo 80:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
4 Choncho anatumiza anthu ku Silo kukatenga likasa la pangano la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene amakhala pamwamba* pa akerubi.+ Ana awiri a Eli, Hofeni ndi Pinihasi,+ analinso komweko limodzi ndi likasa la pangano la Mulungu woona.