-
Numeri 8:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kuti uwayeretse uchite izi: Uwawaze madzi oyeretsera machimo ndipo iwo amete thupi lonse ndi lezala. Komanso achape zovala zawo nʼkudziyeretsa.+
-