-
Numeri 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Asilikali onse a gulu la Yuda amene analembedwa mayina alipo 186,400. Amenewa azikhala oyamba kunyamuka.+
-
-
Numeri 2:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Asilikali onse a gulu la Rubeni amene analembedwa mayina alipo 151,450. Amenewa azikhala achiwiri kunyamuka.+
17 Posamutsa chihema chokumanako,+ gulu la Alevi lizikhala pakati pa magulu enawo.
Dongosolo limene azitsatira posamuka,+ ndi limenenso azitsatira pomanga misasa yawo, aliyense pamalo ake, mogwirizana ndi gulu lawo la mafuko atatu.
-
-
Numeri 2:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Asilikali onse a gulu la Efuraimu amene anawalemba mayina alipo 108,100. Amenewa azikhala achitatu kunyamuka.+
-
-
Numeri 2:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Asilikali onse a gulu la Dani amene analembedwa mayina alipo 157,600. Amenewa azikhala omalizira kunyamuka,+ mogwirizana ndi magulu a Aisiraeli a mafuko atatuatatu.”
-