-
Numeri 12:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno Yehova anatsika mʼchipilala chamtambo+ nʼkuima pakhomo la chihema chokumanako. Kenako anaitana Aroni ndi Miriamu ndipo onse anapita.
-
-
Deuteronomo 31:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiyeno Yehova anaonekera kuchihemako mʼchipilala cha mtambo chimene chinaima pafupi ndi khomo la chihema.+
-