Salimo 99:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ankalankhula nawo kuchokera mʼchipilala cha mtambo.+ Iwo anasunga zikumbutso zake ndi malamulo amene anawapatsa.+
7 Mulungu ankalankhula nawo kuchokera mʼchipilala cha mtambo.+ Iwo anasunga zikumbutso zake ndi malamulo amene anawapatsa.+