-
Salimo 78:26, 27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Anachititsa kuti mphepo yakumʼmawa iwombe mumlengalenga,
Komanso ndi mphamvu zake, anachititsa kuti mphepo yakumʼmwera iwombe.+
27 Iye anawagwetsera nyama yochuluka ngati fumbi,
Anawagwetsera mbalame zochuluka ngati mchenga wamʼmbali mwa nyanja.
-