Numeri 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kuchigwa cha Esikolo,*+ anadula nthambi yokhala ndi phava limodzi lalikulu la mphesa, ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi ndodo yonyamulira. Anatengakonso makangaza* ndi nkhuyu.+
23 Atafika kuchigwa cha Esikolo,*+ anadula nthambi yokhala ndi phava limodzi lalikulu la mphesa, ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi ndodo yonyamulira. Anatengakonso makangaza* ndi nkhuyu.+