-
Oweruza 1:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho fuko la Yuda linapita kukamenyana ndi Akanani amene ankakhala ku Heburoni, (poyamba dzina la mzinda wa Heburoni linali Kiriyati-ariba). Iwo anapha Sesai, Ahimani ndi Talimai.+
-