-
Deuteronomo 1:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Iwo anatengako zina mwa zipatso zamʼdzikolo nʼkutibweretsera, ndipo anatiuza kuti, ‘Dziko limene Yehova Mulungu wathu akufuna kutipatsa ndi labwino.’+
-