Levitiko 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati akupereka nsembe chifukwa cha lonjezo limene anapanga+ kapena ngati akupereka nsembe yaufulu,+ aziidya pa tsiku limene wapereka nsembeyo, ndipo yotsala angathenso kuidya pa tsiku lotsatira.
16 Ngati akupereka nsembe chifukwa cha lonjezo limene anapanga+ kapena ngati akupereka nsembe yaufulu,+ aziidya pa tsiku limene wapereka nsembeyo, ndipo yotsala angathenso kuidya pa tsiku lotsatira.