Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Numeri 1:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Nthawi zonse mukamasamutsa chihema, Aleviwo azichipasula,+ ndipo mukafika pomanga msasa, Alevi ndi amene azimanga chihemacho. Munthu aliyense amene si Mlevi akayandikira chihemacho aziphedwa.+

  • Numeri 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Uike Aroni ndi ana ake kuti akhale ansembe, ndipo azigwira ntchito zawo zaunsembe.+ Munthu wamba* aliyense amene wayandikira malowo, aziphedwa.”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani