-
Levitiko 27:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mundawo ukamadzabwezedwa mʼChaka cha Ufulu, udzakhala wopatulika kwa Yehova monga munda umene waperekedwa kwa iye. Mundawo udzakhala wa ansembe.+
-
-
Levitiko 27:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Koma zinthu zimene munthu wapereka kwa Yehova monga zinthu zoyenera kuwonongedwa, kuchokera pa katundu wake, sizikuyenera kugulitsidwa kapena kuwomboledwa, kaya ndi munthu, nyama kapena munda. Chinthu chilichonse chimene munthu wapereka kwa Yehova ndi chopatulika koposa.+
-