-
Levitiko 22:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Musamapereke nsembe nyama iliyonse yachilema,+ chifukwa Mulungu sangasangalale nanu.
-
-
Malaki 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 “Wotembereredwa ndi aliyense wochita zachinyengo, amene ali ndi nyama yabwinobwino yamphongo pa ziweto zake koma amalonjeza nʼkupereka nsembe nyama yachilema kwa Yehova. Ine ndine Mfumu yaikulu+ ndipo dzina langa lidzaopedwa pakati pa anthu a mitundu ina,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+
-