Numeri 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno munthu amene si wodetsedwa awole phulusa la ngʼombeyo+ nʼkukalisiya pamalo oyera kunja kwa msasawo. Aisiraeli onse azisunga phulusalo kuti aziligwiritsa ntchito pokonza madzi oyeretsera.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo.
9 Ndiyeno munthu amene si wodetsedwa awole phulusa la ngʼombeyo+ nʼkukalisiya pamalo oyera kunja kwa msasawo. Aisiraeli onse azisunga phulusalo kuti aziligwiritsa ntchito pokonza madzi oyeretsera.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo.