-
Salimo 78:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Iye anangʼamba miyala mʼchipululu,
Anawalola kumwa madziwo mpaka ludzu kutha ngati kuti akumwa madzi amʼnyanja.+
-
-
Salimo 114:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Amene amasintha thanthwe kukhala dambo la madzi,
Komanso mwala wa nsangalabwi kukhala akasupe a madzi.+
-