-
Numeri 14:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Zitatero Aamaleki ndi Akanani omwe ankakhala kudera lamapirilo anatsika nʼkuyamba kuwapha ndi kuwabalalitsa mpaka ku Horima.+
-