-
Numeri 16:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kodi ukuyesa nʼchinthu chachingʼono kuti unatichotsa mʼdziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere mʼchipululu muno?+ Kodi tsopano ukufunanso kuti ukhale mfumu yomatilamulira?
-