-
Numeri 2:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Aisiraeli azikhoma matenti awo, pamalo amene gulu lawo la mafuko atatu+ lapatsidwa, munthu aliyense azikhala pafupi ndi chizindikiro cha nyumba ya makolo ake. Iwo azikhoma matenti awo mozungulira chihema chokumanako komanso moyangʼana chihemacho.
-