-
1 Mbiri 6:77Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
77 Kuchokera ku fuko la Zebuloni,+ anapatsa anthu a ku banja la Merari amene anatsala, mzinda wa Rimono ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Tabori ndi malo ake odyetserako ziweto.
-