Numeri 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopano ana a Rubeni+ ndi ana a Gadi+ anali ndi ziweto zambiri ndipo anaona kuti dera la Yazeri+ komanso la Giliyadi, anali malo abwino a ziweto.
32 Tsopano ana a Rubeni+ ndi ana a Gadi+ anali ndi ziweto zambiri ndipo anaona kuti dera la Yazeri+ komanso la Giliyadi, anali malo abwino a ziweto.