-
Yoswa 24:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Aisiraeli. Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori kuti akutemberereni.+
-
-
Oweruza 11:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Ndiye iweyo wasiyana pati ndi Balaki+ mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu? Kodi iye anakwanitsa kulimbana ndi Aisiraeli, kapena anayesa nʼkomwe kumenyana nawo?
-