-
Numeri 22:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Balamu atamva mawuwo anawauza kuti: “Mugone konkuno, ndiyeno ndikuyankhani mogwirizana ndi zimene Yehova angandiuze.” Choncho akalonga a ku Mowabuwo anagonadi kwa Balamu.
-