-
Numeri 22:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma Balamu anayankha atumiki a Balakiwo kuti: “Ngakhale Balaki atandipatsa nyumba yake yodzaza siliva ndi golide, sindingachite chilichonse chosemphana ndi zimene Yehova Mulungu wanga angandilamule, kaya chachingʼono kapena chachikulu.+
-