Numeri 22:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Balamu anayankha Balaki kuti: “Si ine ndabwerane! Koma kodi ndikuloledwa kunena chilichonse? Inetu ndilankhula mawu okhawo amene Mulungu angandiuze.”*+ Numeri 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
38 Balamu anayankha Balaki kuti: “Si ine ndabwerane! Koma kodi ndikuloledwa kunena chilichonse? Inetu ndilankhula mawu okhawo amene Mulungu angandiuze.”*+