Numeri 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atachoka ku Bamoti anapita kuchigwa chimene chili mʼdziko la Mowabu,+ pafupi ndi chitunda cha Pisiga+ chimene chinayangʼanizana ndi dera la Yesimoni.*+
20 Atachoka ku Bamoti anapita kuchigwa chimene chili mʼdziko la Mowabu,+ pafupi ndi chitunda cha Pisiga+ chimene chinayangʼanizana ndi dera la Yesimoni.*+