-
Numeri 22:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Mʼmawa kutacha, Balaki anakatenga Balamu nʼkupita naye ku Bamoti-baala. Anapita naye kumeneko kuti akathe kuliona bwino gulu lonse la Aisiraeli.+
-
-
Numeri 23:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Kenako Balamu anauza Balaki kuti: “Mumange maguwa ansembe okwanira 7+ pamalo ano. Mukatero mundikonzere ngʼombe zamphongo 7 ndi nkhosa zamphongo 7.”
-