-
Numeri 24:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Mawu a munthu amene wamva mawu a Mulungu,
Amene akudziwa Wamʼmwambamwamba,
Anaona masomphenya a Wamphamvuyonse,
Atagwada pansi, maso ake ali otsegula. Mawu ake akuti:
-