-
Numeri 22:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 ‘Taonani! Anthu amene achokera ku Iguputo aja adzaza dziko lonse lapansi kumene munthu angayangʼane. Tsopano bwerani, mudzatemberere anthuwa.+ Mwina ndingathe kumenyana nawo nʼkuwathamangitsa.’”
-