-
Ezekieli 27:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Zopalasira zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana,
Ndipo mbali yakutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, nʼkuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+
-