32 Ana amene Ketura+ mkazi wamngʼono wa Abulahamu anabereka, anali Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+
Ana a Yokesani anali Sheba ndi Dedani.+
33 Ana a Midiyani anali Efa,+ Eferi, Hanoki, Abida ndi Elida.
Onsewa anali ana aamuna a Ketura.