-
Yoswa 13:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Tsopano Yoswa anali atakalamba, ndipo anali ndi zaka zambiri.+ Choncho Yehova anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba ndipo uli ndi zaka zambiri, koma madera oti alandidwe adakali ambiri.
-
-
1 Mafumu 9:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Anamanganso mizinda yake yonse yosungirako zinthu, mizinda yosungirako magaleta,+ mizinda ya amuna okwera pamahatchi ndiponso zilizonse zimene iye anafuna kumanga ku Yerusalemu, ku Lebanoni ndi mʼmadera onse amene ankalamulira.
-