-
Numeri 20:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Gulu lonse la anthuwo litaona kuti Aroni wamwalira, nyumba yonse ya Isiraeli inalira maliro a Aroni kwa masiku 30.+
-