-
Yoswa 13:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mose mtumiki wa Yehova anapereka cholowa kwa hafu ina ya fuko la Manase, kwa fuko la Rubeni ndi kwa fuko la Gadi, kutsidya lakumʼmawa kwa mtsinje wa Yorodano.+
-