23 Muzidzadya chakhumi cha mbewu zanu, kumwa vinyo wanu watsopano, kudya mafuta anu, ana oyamba a ngʼombe ndi a nkhosa zanu pamaso pa Yehova Mulungu wanu, pamalo amene iye adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Muzidzachita zimenezi kuti mudzaphunzire kuopa Yehova Mulungu wanu nthawi zonse.+