Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Musawaope amenewo, chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akukumenyerani nkhondo.’+

  • Deuteronomo 31:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pangʼono.”+

  • Salimo 20:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ena amadalira magaleta ndipo ena amadalira mahatchi,+

      Koma ife timadalira dzina la Yehova Mulungu wathu.+

  • Miyambo 21:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani