Deuteronomo 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova Mulungu wanu adzakudalitsani mogwirizana ndi zimene anakulonjezani ndipo mitundu yambiri idzakongola zinthu zanu,* koma inu simudzafunika kukongola kanthu.+ Mudzalamulira mitundu yambiri koma mitunduyo sidzakulamulirani.+
6 Yehova Mulungu wanu adzakudalitsani mogwirizana ndi zimene anakulonjezani ndipo mitundu yambiri idzakongola zinthu zanu,* koma inu simudzafunika kukongola kanthu.+ Mudzalamulira mitundu yambiri koma mitunduyo sidzakulamulirani.+