-
Maliro 2:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Maso anga atopa ndi kugwetsa misozi.+
Mʼmimba mwanga mukubwadamuka.
-
-
Maliro 2:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Nyamuka! Lira mofuula usiku, pa nthawi yoyamba ulonda.
Khuthula mtima wako pamaso pa Yehova ngati madzi.
Pemphera utakweza manja ako kwa iye chifukwa cha ana ako,
Amene akukomoka ndi njala pamphambano za misewu yonse.+
-