-
1 Samueli 18:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Zimenezi zinangochititsanso kuti Sauli azimuopa kwambiri Davide ndipo Sauli anakhala mdani wa Davide moyo wake wonse.+
-
-
1 Samueli 23:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mukafufuze nʼkudziwa malo onse obisika kumene iye akubisala, ndipo mukabwere ndi umboni. Kenako ndidzapita nanu ndipo ngati alidi kumeneko, ndidzamʼfufuza pakati pa anthu masauzande* a ku Yuda.”
-