1 Mbiri 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Asiriya ataona kuti agonjetsedwa ndi Aisiraeli, anatuma anthu kukaitana Asiriya amene anali mʼdera la ku Mtsinje*+ ndipo Sofaki, mkulu wa asilikali a Hadadezeri, ndi amene ankawatsogolera.+
16 Asiriya ataona kuti agonjetsedwa ndi Aisiraeli, anatuma anthu kukaitana Asiriya amene anali mʼdera la ku Mtsinje*+ ndipo Sofaki, mkulu wa asilikali a Hadadezeri, ndi amene ankawatsogolera.+