2 Samueli 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Davide atafika pamwamba pa phiri, pomwe anthu ankapita kukalambira Mulungu, anaona Husai+ mbadwa ya Areki+ akubwera kudzakumana naye, atangʼamba mkanjo wake ndiponso atadzithira dothi kumutu. 2 Samueli 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Husai+ mbadwa ya Areki,+ mnzake wa Davide, atafika kwa Abisalomu anauza Abisalomu kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”
32 Davide atafika pamwamba pa phiri, pomwe anthu ankapita kukalambira Mulungu, anaona Husai+ mbadwa ya Areki+ akubwera kudzakumana naye, atangʼamba mkanjo wake ndiponso atadzithira dothi kumutu.
16 Husai+ mbadwa ya Areki,+ mnzake wa Davide, atafika kwa Abisalomu anauza Abisalomu kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”