Miyambo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtima wa mfumu uli ngati mitsinje yamadzi mʼdzanja la Yehova.+ Amaupititsa kulikonse kumene iye akufuna.+
21 Mtima wa mfumu uli ngati mitsinje yamadzi mʼdzanja la Yehova.+ Amaupititsa kulikonse kumene iye akufuna.+