Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Samueli 15:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kenako Davide anauzidwa kuti: “Ahitofeli nayenso ali mʼgulu la anthu amene akukonza chiwembu+ ndi Abisalomu.”+ Davide atamva zimenezi anati: “Chonde Yehova,+ chititsani kuti malangizo a Ahitofeli akhale opusa.”+

  • 2 Samueli 15:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Koma ubwerere kumzinda ndipo ukauze Abisalomu kuti, ‘Mfumu, ine ndine mtumiki wanu. Poyamba ndinali mtumiki wa bambo anu koma tsopano ndine mtumiki wanu.’+ Ukakatero, ukatha kunditsutsira malangizo a Ahitofeli.+

  • 2 Samueli 16:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pa nthawiyo, malangizo a Ahitofeli+ ankaonedwa ngati mawu ochokera kwa Mulungu woona. Umu ndi mmene Davide ndi Abisalomu ankaonera malangizo onse a Ahitofeli.

  • Miyambo 19:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Miyambo 21:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira, kapena malangizo amene angalepheretse zimene Yehova amafuna.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani