-
2 Samueli 8:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Zadoki+ mwana wa Ahitubu ndi Ahimeleki mwana wa Abiyatara anali ansembe, ndipo Seraya anali mlembi.
-
-
2 Samueli 15:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Zadoki ndi Abiyatara omwe ndi ansembe ali komweko. Chilichonse chimene ukamve kunyumba ya mfumu ukauze Zadoki ndi Abiyatara.+
-