Salimo 35:24, 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Inu Yehova Mulungu wanga, mundiweruze mogwirizana ndi mfundo zanu zolungama,+Musalole kuti adani anga asangalale chifukwa cha mavuto anga. 25 Musalole kuti mumtima mwawo anene kuti: “Eya! Tapeza zimene timafuna.” Ndipo asanene kuti: “Tamumeza.”+
24 Inu Yehova Mulungu wanga, mundiweruze mogwirizana ndi mfundo zanu zolungama,+Musalole kuti adani anga asangalale chifukwa cha mavuto anga. 25 Musalole kuti mumtima mwawo anene kuti: “Eya! Tapeza zimene timafuna.” Ndipo asanene kuti: “Tamumeza.”+