-
1 Mafumu 1:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Asanamalize kulankhula, kunabwera Yonatani+ mwana wa wansembe Abiyatara. Ndipo Adoniya anati: “Lowa, iwe ndiwe munthu wabwino ndipo uyenera kuti wabweretsa nkhani yabwino.”
-