2 Samueli 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Samueli 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Iwo alinso ndi ana awo awiri komweko, Ahimazi+ mwana wa Zadoki ndi Yonatani+ mwana wa Abiyatara. Ndiye mukatume ana awowo kuti adzandiuze zonse zimene mungamve.” 2 Samueli 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Ahimazi+ mwana wa Zadoki anati: “Bwanji ndithamange ndikapereke uthengawu kwa mfumu, chifukwa Yehova wachitira mfumu chilungamo poilanditsa mʼmanja mwa adani ake?”+
36 Iwo alinso ndi ana awo awiri komweko, Ahimazi+ mwana wa Zadoki ndi Yonatani+ mwana wa Abiyatara. Ndiye mukatume ana awowo kuti adzandiuze zonse zimene mungamve.”
19 Ndiyeno Ahimazi+ mwana wa Zadoki anati: “Bwanji ndithamange ndikapereke uthengawu kwa mfumu, chifukwa Yehova wachitira mfumu chilungamo poilanditsa mʼmanja mwa adani ake?”+